Cinely

Nkhadze Drama Stories

@nkhadze

11 followers · 1 series

image 1 it's Finias Nkhadze .Sali osangalala chifukwa bambo Ake adaphedwa ndi zigawenga. image 2 ndi James iye ndi mafia wagulu limene lidapha bambo a Finias. Ndiwankhaza kwambiri. Image 3 ndi twin brother wa Finias Nkhadze iyeyu ndi Hussein Nkhadze iye adaleledwa ndi ankolo ake ndipo adali achuma ndipo adaphunzira amakhala mosangalala Iyeyu ndi twin brother wake sankadziwana mpaka atakula

Follow creators in the Cinely app

Get notified the moment they publish something new.

  • HD, no watermark
  • Save to your device
  • Create faster

Series